Yeremiya 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo ndidzatenga zinthu zonse zosungidwa mumzindawu, katundu wawo yense, zinthu zonse zamtengo wapatali ndi chuma chonse cha mafumu a Yuda, n’kuzipereka m’manja mwa adani awo.+ Ndipo adaniwo adzafunkha zinthu zimenezi ndi kupita nazo ku Babulo.+
5 Ndipo ndidzatenga zinthu zonse zosungidwa mumzindawu, katundu wawo yense, zinthu zonse zamtengo wapatali ndi chuma chonse cha mafumu a Yuda, n’kuzipereka m’manja mwa adani awo.+ Ndipo adaniwo adzafunkha zinthu zimenezi ndi kupita nazo ku Babulo.+