Salimo 44:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwagulitsa anthu anu pa mtengo wotsika kwambiri,+Ndipo simunapeze phindu ndi mtengo wawo. Yesaya 52:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu inu munagulitsidwa popanda malipiro alionse,+ ndipo mudzawomboledwanso popanda ndalama.”+
3 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu inu munagulitsidwa popanda malipiro alionse,+ ndipo mudzawomboledwanso popanda ndalama.”+