Deuteronomo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+ N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka. Yesaya 52:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu inu munagulitsidwa popanda malipiro alionse,+ ndipo mudzawomboledwanso popanda ndalama.”+
30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+ N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.
3 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu inu munagulitsidwa popanda malipiro alionse,+ ndipo mudzawomboledwanso popanda ndalama.”+