Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+

  • 1 Samueli 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atatero iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anawagulitsa+ kwa Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anapitiriza kumenyana nawo.

  • Salimo 44:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mwagulitsa anthu anu pa mtengo wotsika kwambiri,+

      Ndipo simunapeze phindu ndi mtengo wawo.

  • Yesaya 50:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Yehova wanena kuti: “Kodi anthu inu, chili kuti chikalata chothetsera ukwati+ wa mayi wanu yemwe ndinamuthamangitsa?+ Kapena kodi anthu inu ndakugulitsani+ kwa munthu uti amene ndinali naye ngongole? Inutu mwagulitsidwa chifukwa cha zolakwa zanu,+ ndipo mayi wanu wathamangitsidwa chifukwa cha zochimwa zanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena