Oweruza 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+ Oweruza 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ana a Isiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ moti Yehova anawapereka m’manja mwa Afilisiti+ zaka 40.
7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+
13 Tsopano ana a Isiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ moti Yehova anawapereka m’manja mwa Afilisiti+ zaka 40.