Deuteronomo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+
24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+