Mateyu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Afarisi anabwera kwa iye, ndipo pofuna kumuyesa anamufunsa kuti: “Kodi n’kololeka kuti mwamuna asiye mkazi wake pa chifukwa chilichonse?”+ Mateyu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anayankha kuti: “Chifukwa cha kuuma mtima kwanu,+ Mose anakulolezani kuti muzithetsa ukwati, koma kuyambira pa chiyambi sizinali choncho ayi.+
3 Afarisi anabwera kwa iye, ndipo pofuna kumuyesa anamufunsa kuti: “Kodi n’kololeka kuti mwamuna asiye mkazi wake pa chifukwa chilichonse?”+
8 Iye anayankha kuti: “Chifukwa cha kuuma mtima kwanu,+ Mose anakulolezani kuti muzithetsa ukwati, koma kuyambira pa chiyambi sizinali choncho ayi.+