Deuteronomo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+ Mateyu 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Afarisi+ ndi Asaduki anafika kwa Yesu. Pofuna kumuyesa, anam’pempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+ Maliko 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano kunafika Afarisi. Pofuna kumuyesa, anayamba kumufunsa ngati n’kololeka kuti mwamuna asiye mkazi wake.+
24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+
16 Kenako Afarisi+ ndi Asaduki anafika kwa Yesu. Pofuna kumuyesa, anam’pempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+
2 Tsopano kunafika Afarisi. Pofuna kumuyesa, anayamba kumufunsa ngati n’kololeka kuti mwamuna asiye mkazi wake.+