Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+