Mateyu 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Afarisi+ ndi Asaduki anafika kwa Yesu. Pofuna kumuyesa, anam’pempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+ Maliko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+ Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Ayudawo anati: “Utionetsa chizindikiro+ chotani tsopano chosonyeza kuti uli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi?” 1 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Ayuda amafuna kuona zizindikiro+ ndipo Agiriki amafunafuna nzeru,+
16 Kenako Afarisi+ ndi Asaduki anafika kwa Yesu. Pofuna kumuyesa, anam’pempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+
11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+
18 Koma Ayudawo anati: “Utionetsa chizindikiro+ chotani tsopano chosonyeza kuti uli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi?”