Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+ Luka 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamene anthu osonkhana pamodzi anali kuchulukirachulukira, iye anayamba kunena kuti: “M’badwo uwu ndi m’badwo woipa, ukufuna chizindikiro.+ Koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.+
29 Pamene anthu osonkhana pamodzi anali kuchulukirachulukira, iye anayamba kunena kuti: “M’badwo uwu ndi m’badwo woipa, ukufuna chizindikiro.+ Koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.+