Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+ Mateyu 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Afarisi+ ndi Asaduki anafika kwa Yesu. Pofuna kumuyesa, anam’pempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+ Yohane 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro+ chotani, kuti ife tichione, ndi kukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?
16 Kenako Afarisi+ ndi Asaduki anafika kwa Yesu. Pofuna kumuyesa, anam’pempha kuti awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba.+
30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro+ chotani, kuti ife tichione, ndi kukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?