Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+ Maliko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho anadzuma mowawidwa mtima+ ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani m’badwo umenewu ukufunitsitsa chizindikiro? Ndithu ndikukuuzani, M’badwo umenewu sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse.”+ Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Ayudawo anati: “Utionetsa chizindikiro+ chotani tsopano chosonyeza kuti uli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi?” 1 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Ayuda amafuna kuona zizindikiro+ ndipo Agiriki amafunafuna nzeru,+
12 Choncho anadzuma mowawidwa mtima+ ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani m’badwo umenewu ukufunitsitsa chizindikiro? Ndithu ndikukuuzani, M’badwo umenewu sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse.”+
18 Koma Ayudawo anati: “Utionetsa chizindikiro+ chotani tsopano chosonyeza kuti uli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi?”