Maliko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+ Luka 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ena pofuna kumuyesa, anayamba kumupempha kuti awasonyeze chizindikiro+ chochokera kumwamba. 1 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Ayuda amafuna kuona zizindikiro+ ndipo Agiriki amafunafuna nzeru,+
11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+