Luka 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ena pofuna kumuyesa, anayamba kumukakamiza kuti awasonyeze chizindikiro+ chochokera kumwamba.
16 Koma ena pofuna kumuyesa, anayamba kumukakamiza kuti awasonyeze chizindikiro+ chochokera kumwamba.