Luka 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ena pofuna kumuyesa, anayamba kumupempha kuti awasonyeze chizindikiro+ chochokera kumwamba.