Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+ Maliko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+ 1 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Ayuda amafuna kuona zizindikiro+ ndipo Agiriki amafunafuna nzeru,+
11 Kumeneku kunafika Afarisi ndipo anayamba kutsutsana naye. Ankafuna kuti iye awaonetse chizindikiro chochokera kumwamba, pofuna kumuyesa.+