Deuteronomo 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munaiwala Thanthwe limene linakuberekani,+Ndipo munayamba kuiwala Mulungu amene anachititsa kuti mukhalepo kudzera mwa zowawa za pobereka.+ Oweruza 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+ Salimo 106:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iwo anakhala odetsedwa chifukwa cha ntchito zawo,+Zochita zawo zinawalowetsa m’makhalidwe oipa.+
18 Munaiwala Thanthwe limene linakuberekani,+Ndipo munayamba kuiwala Mulungu amene anachititsa kuti mukhalepo kudzera mwa zowawa za pobereka.+
12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+