Yesaya 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+ chifukwa alambalala malamulo,+ asintha malamulowo+ ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.+ Ezekieli 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ndinauza ana awo m’chipululu kuti,+ ‘Musayende motsatira malamulo a makolo anu,+ ndipo musasunge zigamulo zawo.+ Musadziipitse ndi mafano awo onyansa.+
5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+ chifukwa alambalala malamulo,+ asintha malamulowo+ ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.+
18 Choncho ndinauza ana awo m’chipululu kuti,+ ‘Musayende motsatira malamulo a makolo anu,+ ndipo musasunge zigamulo zawo.+ Musadziipitse ndi mafano awo onyansa.+