Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+ 1 Petulo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pajatu mukudziwa kuti sizinali zinthu zotha kuvunda,+ siliva kapena golide, zimene zinakumasulani+ ku khalidwe lanu lopanda phindu limene munalilandira kuchokera kwa makolo anu mwa chikhalidwe chanu.
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
18 Pajatu mukudziwa kuti sizinali zinthu zotha kuvunda,+ siliva kapena golide, zimene zinakumasulani+ ku khalidwe lanu lopanda phindu limene munalilandira kuchokera kwa makolo anu mwa chikhalidwe chanu.