Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+ Ezekieli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti anthu inu munali ovuta+ kuposa mitundu imene yakuzungulirani, ndipo simunayende m’malamulo anga, komanso simunatsatire zigamulo zanga,+ koma munatsatira zigamulo za mitundu imene yakuzungulirani,+
8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+
7 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti anthu inu munali ovuta+ kuposa mitundu imene yakuzungulirani, ndipo simunayende m’malamulo anga, komanso simunatsatire zigamulo zanga,+ koma munatsatira zigamulo za mitundu imene yakuzungulirani,+