2 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa. Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu wa anthu umene unasinthanitsapo milungu yawo+ ndi zinthu zimene kwa iwo si milungu yeniyeni?+ Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zosapindulitsa.+ Ezekieli 16:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwe sikuti unangoyenda chabe m’njira zawo ndiponso sikuti unangochita zinthu motsatira zinthu zawo zonyansa,+ koma m’nthawi yochepa unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa iwowo m’njira zako zonse.+
11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa.
11 Kodi pali mtundu wa anthu umene unasinthanitsapo milungu yawo+ ndi zinthu zimene kwa iwo si milungu yeniyeni?+ Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zosapindulitsa.+
47 Iwe sikuti unangoyenda chabe m’njira zawo ndiponso sikuti unangochita zinthu motsatira zinthu zawo zonyansa,+ koma m’nthawi yochepa unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa iwowo m’njira zako zonse.+