2 Mafumu 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene unayakira Yuda,+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anawachititsa, n’kukwiyitsa nazo Mulungu.+ 2 Mafumu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimenezi zinachitikira Yuda molamulidwa ndi Yehova, kuti achotse+ dzikolo pamaso pake chifukwa cha machimo a Manase,+ malinga ndi zonse zimene anachita, Yeremiya 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho,+ chifukwa cha zimene Manase, mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+
26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene unayakira Yuda,+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anawachititsa, n’kukwiyitsa nazo Mulungu.+
3 Zimenezi zinachitikira Yuda molamulidwa ndi Yehova, kuti achotse+ dzikolo pamaso pake chifukwa cha machimo a Manase,+ malinga ndi zonse zimene anachita,
4 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho,+ chifukwa cha zimene Manase, mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+