2 Mafumu 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa za mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli. 2 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa. 2 Mafumu 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene unayakira Yuda,+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anawachititsa, n’kukwiyitsa nazo Mulungu.+
2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa za mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.
11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa.
26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene unayakira Yuda,+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anawachititsa, n’kukwiyitsa nazo Mulungu.+