Levitiko 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mukapewa kuchita zimenezi, dziko silidzakusanzani chifukwa choliipitsa mmene lidzasanzira mitundu imene ikukhalamo musanafike inu.+ Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ 2 Mbiri 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa+ za mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+
28 Mukapewa kuchita zimenezi, dziko silidzakusanzani chifukwa choliipitsa mmene lidzasanzira mitundu imene ikukhalamo musanafike inu.+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa+ za mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+