2 Mafumu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ahazi anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake monga anachitira Davide kholo lake.+
2 Ahazi anali ndi zaka 20 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wake monga anachitira Davide kholo lake.+