51 “‘Komanso, Samariya+ sanachite machimo ofika ngakhale hafu ya machimo ako. Koma iwe unapitiriza kuchulukitsa zinthu zako zonyansa kuposa abale ako, moti unachititsa kuti iwo aoneke ngati olungama chifukwa cha zinthu zako zonse zonyansa zimene unali kuchita.+