Yeremiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova anapitiriza kundiuza kuti: “Isiraeli wosakhulupirikayo wakhala wolungama kuposa Yuda wochita zachinyengoyo.+ Mateyu 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anthu a ku Nineve adzaimirira pa chiweruzo limodzi ndi m’badwo uwu+ ndipo adzautsutsa,+ chifukwa iwo analapa atamva ulaliki wa Yona.+ Koma tsopano wina woposa Yona ali pano.
11 Yehova anapitiriza kundiuza kuti: “Isiraeli wosakhulupirikayo wakhala wolungama kuposa Yuda wochita zachinyengoyo.+
41 Anthu a ku Nineve adzaimirira pa chiweruzo limodzi ndi m’badwo uwu+ ndipo adzautsutsa,+ chifukwa iwo analapa atamva ulaliki wa Yona.+ Koma tsopano wina woposa Yona ali pano.