Levitiko 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite+ zimene amachita anthu a ku Iguputo kumene munali kukhala, ndipo musakachite+ zimene amachita m’dziko la Kanani, kumene ndikukulowetsani. Musakatsatire mfundo zawo. Deuteronomo 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Musapembedze Yehova Mulungu wanu m’njira imeneyi,+
3 Musachite+ zimene amachita anthu a ku Iguputo kumene munali kukhala, ndipo musakachite+ zimene amachita m’dziko la Kanani, kumene ndikukulowetsani. Musakatsatire mfundo zawo.