2 Mafumu 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wansembe Uliya+ anamanga guwa lansembelo.+ Analimanga mogwirizana ndi zonse zimene Mfumu Ahazi inam’tumizira kuchokera ku Damasiko, podikira kuti Mfumu Ahazi ibwereko ku Damasiko.
11 Wansembe Uliya+ anamanga guwa lansembelo.+ Analimanga mogwirizana ndi zonse zimene Mfumu Ahazi inam’tumizira kuchokera ku Damasiko, podikira kuti Mfumu Ahazi ibwereko ku Damasiko.