Yesaya 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna mboni zokhulupirika kuti zindichitire umboni.+ Mbonizo zikhale wansembe Uriya+ ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.”
2 Ndikufuna mboni zokhulupirika kuti zindichitire umboni.+ Mbonizo zikhale wansembe Uriya+ ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.”