2 Mafumu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Mfumu Ahazi+ inapita kukakumana ndi Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ku Damasiko. Kumeneko inaonako guwa lansembe,+ chotero Mfumu Ahazi inatumizira wansembe Uliya chitsanzo cha kamangidwe ka guwa lansembe lonselo.+
10 Kenako Mfumu Ahazi+ inapita kukakumana ndi Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ku Damasiko. Kumeneko inaonako guwa lansembe,+ chotero Mfumu Ahazi inatumizira wansembe Uliya chitsanzo cha kamangidwe ka guwa lansembe lonselo.+