Genesis 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma m’badwo wachinayi udzabwerera kuno,+ chifukwa nthawi yoti Aamori alangidwe sinakwane.”+ Levitiko 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiye chifukwa chake dzikolo n’lodetsedwa, ndipo ndidzalilanga chifukwa cha kulakwa kwake. Pamenepo dzikolo lidzataya anthu ake kunja.+ Ezekieli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akunena kwa iwe Yerusalemu kuti: “Iwe unachokera kudziko la Akanani ndipo unabadwira komweko.+ Bambo ako anali Muamori,+ mayi ako anali Mhiti.+
25 Ndiye chifukwa chake dzikolo n’lodetsedwa, ndipo ndidzalilanga chifukwa cha kulakwa kwake. Pamenepo dzikolo lidzataya anthu ake kunja.+
3 Umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akunena kwa iwe Yerusalemu kuti: “Iwe unachokera kudziko la Akanani ndipo unabadwira komweko.+ Bambo ako anali Muamori,+ mayi ako anali Mhiti.+