1 Mafumu 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri mwa kutsatira mafano onyansa+ monga momwe Aamori, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, anachitira.’”+ 2 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa. 1 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+
26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri mwa kutsatira mafano onyansa+ monga momwe Aamori, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, anachitira.’”+
11 “Manase+ mfumu ya Yuda yachita zinthu zonyansazi.+ Yachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu. Iye wachimwitsa ngakhale Yuda+ ndi mafano ake onyansa.
16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+