Yoswa 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+ Machitidwe 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu anati, ‘Ndidzaweruza mtundu umene adzautumikire monga akapolo,+ pambuyo pake adzatuluka ndi kudzanditumikira m’malo ano.’+
14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+
7 Mulungu anati, ‘Ndidzaweruza mtundu umene adzautumikire monga akapolo,+ pambuyo pake adzatuluka ndi kudzanditumikira m’malo ano.’+