Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 9
11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+