Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu wa anthu umene unasinthanitsapo milungu yawo+ ndi zinthu zimene kwa iwo si milungu yeniyeni?+ Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zosapindulitsa.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 9
11 Kodi pali mtundu wa anthu umene unasinthanitsapo milungu yawo+ ndi zinthu zimene kwa iwo si milungu yeniyeni?+ Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zosapindulitsa.+