Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+ Yesaya 66:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+ Amosi 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu anga onse ochimwa adzaphedwa ndi lupanga.+ Iwo amanena kuti: “Tsoka silitiyandikira kapena kutigwera.”’+
16 Pakuti ngati moto woyaka, Yehova adzaweruza anthu onse ndi lupanga lake,+ ndipo anthu ophedwa ndi Yehova adzakhala ambiri.+
10 Anthu anga onse ochimwa adzaphedwa ndi lupanga.+ Iwo amanena kuti: “Tsoka silitiyandikira kapena kutigwera.”’+