Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeliwo sanamvere+ mawu a Yehova Mulungu wawo, koma anaphwanya pangano lake,+ ngakhalenso zonse zimene Mose+ mtumiki wa Yehova anawalamula.+ Iwo sanamvere kapena kuzichita.

  • Ezekieli 20:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Ndidzachotsa pakati panu anthu ondipandukira ndi ondichimwira.+ Pakuti ndidzawatulutsa m’dziko limene akukhalamo monga alendo, koma sadzalowa m’dziko la Isiraeli,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+

  • Nahumu 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+

      Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena