Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Wosungira mibadwo masauzande kukoma mtima kosatha,+ wokhululukira zolakwa ndi machimo,+ koma wosalekerera konse wolakwa osam’langa.+ Wolanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+

  • Yeremiya 46:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chotero, iwe Yakobo mtumiki wanga usachite mantha, pakuti ine ndili ndi iwe.+ Ine ndidzafafaniza mitundu yonse ya anthu kumene ndakubalalitsirako,+ koma iwe sindidzakufafaniza.+ Ngakhale zili choncho, ndidzakulanga pamlingo woyenera,+ ndipo ndithu sindidzakusiya osakulanga,’+ watero Yehova.”

  • Amosi 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena