Chivumbulutso 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Mulungu anaika izi m’mitima yawo kuti zichite monga mwa maganizo ake,+ kuti zikwaniritse maganizo awo amodzi, mwa kupereka ufumu wawo kwa chilombo,+ kufikira mawu a Mulungu atakwaniritsidwa.+
17 Pakuti Mulungu anaika izi m’mitima yawo kuti zichite monga mwa maganizo ake,+ kuti zikwaniritse maganizo awo amodzi, mwa kupereka ufumu wawo kwa chilombo,+ kufikira mawu a Mulungu atakwaniritsidwa.+