Chivumbulutso 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10+ amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi.
12 “Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10+ amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi.