Danieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+
24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+