Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndinafunanso kudziwa za nyanga 10 zimene zinali pamutu pake+ ndi nyanga ina+ imene inamera, imene inachititsa kuti nyanga zitatu zigwe.+ Nyanga imeneyi inali ndi maso ndi pakamwa polankhula mawu odzitukumula+ ndipo inali kuoneka yaikulu kuposa zinzake zija.

  • Chivumbulutso 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga+ wa m’mbali mwa nyanja.

      Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka m’nyanja.+ Chinali ndi nyanga 10+ ndi mitu 7.+ Kunyanga yake iliyonse kunali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu.+

  • Chivumbulutso 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10+ amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena