Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 57:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Koma anthu oipa ali ngati nyanja imene ikuwinduka, imene ikukanika kukhala bata, imene madzi ake akuvundula zomera za m’nyanjamo ndiponso matope.

  • Danieli 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye anati:

      “M’masomphenya ausiku, ndinaona mphepo zinayi+ zakumwamba zikuvundula nyanja yaikulu.+

  • Habakuku 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 N’chifukwa chiyani mukuchititsa munthu kukhala ngati nsomba zam’nyanja ndiponso ngati zokwawa zam’nyanja zimene zilibe mtsogoleri woziteteza?+

  • Chivumbulutso 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+

  • Chivumbulutso 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano ndinaona kumwamba+ kwatsopano ndi dziko lapansi+ latsopano, pakuti kumwamba+ kwakale ndi dziko lapansi lakale+ zinali zitachoka, ndipo kulibenso nyanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena