Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano Davide anali atakhala pakati pa zipata ziwiri.+ Pa nthawiyi mlonda+ anakwera padenga la mpanda kuchipata. Ndiyeno atakweza maso anaona munthu akuthamanga ali yekha.

  • 2 Mafumu 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ku Yezereeliko,+ mlonda+ amene anaimirira pansanja+ anaona gulu lankhondo la Yehu likubwera mwaliwiro. Nthawi yomweyo mlondayo anati: “Ndikuona gulu la amuna likubwera mwaliwiro.” Pamenepo Yehoramu anati: “Uza munthu wokwera hatchi kuti apite kukakumana nawo. Akawafunse kuti, ‘Kodi mukubwerera zamtendere?’”+

  • Yesaya 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango,+ kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda, ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+

  • Yeremiya 51:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kwezerani mpanda wa Babulo mtengo wa chizindikiro.+ Wonjezerani alonda+ ndipo ikani alondawo pamalo awo. Konzekeretsani omenya nkhondo mobisalira anzawo.+ Pakuti Yehova waganiza zoti achite ndipo adzachitira anthu okhala ku Babulo zimene wanena.”+

  • Hoseya 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pa nthawi ina, mlonda+ wa Efuraimu anali ndi Mulungu wanga.+ Koma tsopano panjira zonse za mneneri,+ pali msampha wa wosaka mbalame.+ M’nyumba ya Mulungu wake muli chidani chachikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena