2 Samueli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mfumu inawauza kuti: “Ndichita zilizonse zimene inu mukuona kuti n’zabwino.”+ Pamenepo mfumu inangoima pambali pa chipata,+ ndipo anthu onse anapita kunkhondo m’magulu a anthu 100 ndi 1,000.+
4 Choncho mfumu inawauza kuti: “Ndichita zilizonse zimene inu mukuona kuti n’zabwino.”+ Pamenepo mfumu inangoima pambali pa chipata,+ ndipo anthu onse anapita kunkhondo m’magulu a anthu 100 ndi 1,000.+