2 Samueli 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Davide anali atakhala pakati pa zipata ziwiri.+ Pa nthawiyi mlonda+ anakwera padenga la mpanda kuchipata. Ndiyeno atakweza maso anaona munthu akuthamanga ali yekha.
24 Tsopano Davide anali atakhala pakati pa zipata ziwiri.+ Pa nthawiyi mlonda+ anakwera padenga la mpanda kuchipata. Ndiyeno atakweza maso anaona munthu akuthamanga ali yekha.