Salimo 134:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene mukupemphera mutakweza manja anu, muzikhala oyera,+Ndipo tamandani Yehova.+ Machitidwe 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Koneliyo anayang’anitsitsa mngelo uja, ndipo mantha atamugwira anati: “N’chiyani Mbuyanga?” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mapemphero ako+ ndi mphatso zako zachifundo zakwera kwa Mulungu monga chikumbutso.+
4 Pamenepo Koneliyo anayang’anitsitsa mngelo uja, ndipo mantha atamugwira anati: “N’chiyani Mbuyanga?” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mapemphero ako+ ndi mphatso zako zachifundo zakwera kwa Mulungu monga chikumbutso.+