Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 28:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,

      Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+

  • Salimo 141:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+

      Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+

  • Maliro 3:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Tiyeni tichonderere Mulungu kumwamba ndi mtima wonse, ndipo tikweze manja athu m’mwamba+ ndi kunena kuti:

  • 2 Akorinto 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ifeyo tili ndi chifukwa chodzitamandira chakuti m’dzikoli, makamaka pakati pa inuyo, tachita zinthu zoyera ndiponso moona mtima mogwirizana ndi zimene Mulungu amaphunzitsa. Tachita zimenezi osati modalira nzeru+ za m’dzikoli koma modalira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, ndipo chikumbumtima chathu chikuchitiranso umboni zimenezi.+

  • 1 Timoteyo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho, ndikufuna kuti kulikonse amuna apitirize kupemphera, kukweza m’mwamba manja awo oyera+ popanda kukwiyirana+ ndi kutsutsana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena